Song: Back To Sender
Year: 2021
Viewed: 64 - Published at: 2 years ago

[Chorus: Eli Njuchi, Kell Kay & Teddy]
Phone umadzangova "hello, man mkazi uja lero"
Zomwe apanga ndimbola
Mamuna aliyense angolola
Munkati mwapeza ka girl, koma mwazinamiza sikam'ngelo
Koma zachimwana, zachibwana mungonamizana
Back to sender
Za ine ndi mkazi wanga ayang'anila ndi Ambuye
(Sender, ah-yeah, ah-yeah, ah yeah)
Back to sender
Zomwe zikanike nzayinu ndi akwanuwo
(Sender, ah-yeah, ah-yeah, ah yeah)
Back to sender

[Verse 1: Charisma]
Is it the fact that we balling?
Or you heard the fact she my darling?
Just because we're shining
Mpaka kumapeka nkhani
So back to sender
Mkazi wanga siwoyendayenda
Mukapitiliza nzakugendani
Mutijeda breda nzosayenda
Ena akathela kujahena
[Refrain: Charisma & Kell Kay]
Zomwe mukupanga ndikuziwa kale
Basi kubwera kufuna kunditchela ndale
Cholinga mkazi wangayo ndimutaye
Mukunama nafe ma guy
Wachitemwa wanga iwe
True lover iwe
Mkazi wanga tisamamvere
Wachikondi wanga iwe
True lover iwe
Mkazi wanga tisamamvere

[Chorus: Eli Njuchi, Kell Kay & Teddy]
Phone umadzangova "hello, man mkazi uja lero"
Zomwe apanga ndimbola
Mamuna aliyense angolola
Munkati mwapeza ka girl, koma mwazinamiza sikam'ngelo
Koma zachimwana, zachibwana mungonamizana
Back to sender
Za ine ndi mkazi wanga ayang'anila ndi Ambuye
(Sender, ah-yeah, ah-yeah, ah yeah)
Back to sender
Zomwe zikanike nzayinu ndi akwanuwo
(Sender, ah-yeah, ah-yeah, ah yeah)
Back to sender
[Verse 2: Charisma]
Komwe tinakumana kunalibeko
Nafusira inu kulibeko
Chonde ndisiyileni Nasibeko
Anandipatsa ndi ambuye kuti eko
E-e-eko, so we take over
Yeah, we like Queen B and Hova
Like Mr Eazy, tell her leg over
She's the only one i can't get over

[Refrain: Charisma & Kell Kay]
Zomwe mukupanga ndikuziwa kale
Basi kubwera kufuna kunditchela ndale
Cholinga mkazi wangayo ndimutaye
Mukunama nafe ma guy
Wachitemwa wanga iwe
True lover iwe
Mkazi wanga tisamamvere
Wachikondi wanga iwe
True lover iwe
Mkazi wanga tisamamvere

[Chorus: Eli Njuchi, Kell Kay & Teddy]
Phone umadzangova "hello, man mkazi uja lero"
Zomwe apanga ndimbola
Mamuna aliyense angolola
Munkati mwapeza ka girl, koma mwazinamiza sikam'ngelo
Koma zachimwana, zachibwana mungonamizana
Back to sender
Za ine ndi mkazi wanga ayang'anila ndi Ambuye
(Sender, ah-yeah, ah-yeah, ah yeah)
Back to sender
Zomwe zikanike nzayinu ndi akwanuwo
(Sender, ah-yeah, ah-yeah, ah yeah)
Back to sender

( Charisma (MW) )
www.ChordsAZ.com

TAGS :