Song: Dear Soulmate
Artist:  Q Cee
Year: 2021
Viewed: 11 - Published at: 9 years ago

[Verse 1]
Hello, kodi ukundimva?
Ndati ndikupatse moni
Ineyo ndati sindi-giver
Mpaka undiyike mu zone
Sindifuna olakwika andikonde
Andizuze mpakana ndiwonde
Vumbuluka komwe uli chonde
Chonde chonde

[Chorus]
Dear soulmate
Ndindani yemwe atipange connect
Imva ndikukuyimbira ka whistle
Vumbuluka komwe uli ndikuthile diso

[Verse 2]
Kapena ufuna ena andiseweletse kaye
Chonde tabwera mwachangu komwe uliko darlie
Kapena ufuna kuti ndiguge kaye
Koma that's not fair, fair
Komano soulmate wanga
Udziwe ukundilanga
Dziwa I'm waiting for you
I'm waiting for you
[Chorus]
Dear soulmate
Ndindani yemwe atipange connect
Imva ndikukuyimbira ka whistle
Vumbuluka komwe uli ndikuthile diso

[Bridge]
Where are you soulmate?
Where are you soulmate?
Where are you soulmate?
Can you hear me?
Can you hear me?

[Chorus]
Dear soulmate
Ndindani yemwe atipange connect
Imva ndikukuyimbira ka whistle
Vumbuluka komwe uli ndikuthile diso
Dear soulmate
Ndindani yemwe atipange connect
Imva ndikukuyimbira ka whistle
Vumbuluka komwe uli ndikuthile diso

( Q Cee )
www.ChordsAZ.com

TAGS :