Song: Ndileke
Year: 2021
Viewed: 12 - Published at: 3 years ago

[Verse 1]
Pomwe ndikufunitsitsa ndipamene wandisiya
Ulibe nazo ntchito olo ntagwera mutu
Sukumva za munthu
Koma ine wandisiya ndi ludzu
Ndimafunabe pang'ono
Pang'ono nkumakuphuzira

[Refrain]
Darlie tulo [?]
Wandikhapila kosathwa
Komano ndayesetsa ndafika potopa
Ati sudzasiya kundikonda, kumawuza anthu ena
Tsono ngati umandikonda bwanji suli ndine?
Tsono taleka ndikuwuze

[Pre-Chorus]
Ndinakupilira mu nzinthu zambiri
Zina zoyipa ndimamva titasiyana
Koma ukati ulile bodza
Uwonetsa kankhope ka m'ngelo
Anzako ena ankandifunsiraso
Ndilibe chipongwe chabe ndinkakana
Koma ukati undiyalutse anzako akuwona
[Chorus]
Basi
Oh, basi ndileke
Basi
Oh, basi ndileke

[Verse 2]
Ngakhale pandekha osandilankhula (No)
Ukakhalakhala osafusa za ine (No)
Ukamagona usalote ine
(Enough is enough, ine ndatopa)
Unandichotsa mtima kuyika mwala
Pano onse ondiwuza amandikonda
Nkawang'ana ndikulira
Unandichotsera umunthu wanga
Tsiku osatha ndilire, ndilire, ndilire

[Refrain]
Ati sudzasiya kundikonda, kumawuza anthu ena
Tsono ngati umandikonda bwanji suli ndine?
Tsono taleka ndikuwuze

[Pre-Chorus]
Ndinakupilira mu nzinthu zambiri
Zina zoyipa ndimamva titasiyana
Koma ukati ulile bodza
Uwonetsa kankhope ka m'ngelo
Anzako ena ankandifunsiraso
Ndilibe chipongwe chabe ndinkakana
Koma ukati undiyalutse anzako akuwona
[Chorus]
Basi
Oh, basi ndileke
Basi
Oh, basi ndileke
Basi
Oh, basi ndileke
Basi
Oh, basi ndileke

( Lulu & Mathumela Band )
www.ChordsAZ.com

TAGS :