Song: Pogona
Year: 2021
Viewed: 25 - Published at: 6 years ago

[Intro]
Yah
Oh-yah-yah
Oh-yah-yah
Oh-yah-yah
Oh-yah-yah

[Chorus]
Amandikonda pogona
Amandifuna pogona
Amandikonda pogona
Amandifuna pogona
Amandikonda pogona, gona
Kunkonda pogona
Amandifuna pogona, gona
Kunfuna pogona

[Verse]
Kumbali amandikana, amati ine ndine hule
Kumbali amandinyoza, ati ndine osauka
Kumbali amandikana, amangoti ndine mzake
Kumbali amandinyoza, ati ndimankakamila
Koma zikamuvuta amabwera kwathu, "Baby ine ndakusowa"
Koma zikamuvuta amabwera kwathu, "Baby ndili nawe nkhani"
Komatu sakamba ayi, amangokhala pa easy
Komatu sa-talker ayi, ndimangodziwa ma PG
Ndimalakalaka nditabweza chipongwe koma ine zimandikanika
Ndimalakalaka nditabweza choyipa koma ine zimandikanika
Ndimamukonda ine, sindifuna atandisiya
Ndimamufila ine, sindifuna ntamusiya
[Chorus]
Komabe, amandikonda pogona
Amandifuna pogona
Amandikonda pogona
Amandifuna pogona
Amandikonda pogona, gona
Kunkonda pogona
Amandifuna pogona, gona
Kunfuna pogona

[Outro]
Yah-yah, yah-yah
Yah-yah, yah-yah
Yah-yah, yah-yah
Yah-yah, yah-yah, prr

( SevenOmore (MW) )
www.ChordsAZ.com

TAGS :