Artist: Phyzix
Lyrics of Artist: Phyzix
Lyrics of Artist: Phyzix
[Lyric] Wife Material (Phyzix)
[Verse 1: Phyzix] Ndinapeza chi bhebhi anthu adziwe Sindimachibisa sichapadziwe Yemwe zikumuwawa adhiwe Koma ichichi ndichanga chilindiwe Sichingadzakupatse mphindi iwe Chimakhala chili ndine udzimva iwe Vito lake iweyo kudzimwa iwe Umangogwila akaza openga ma byzwe Za ife ndizokoma zothila kale Sitimvetsana kuwawa, tsabola wa kale Uyuyu ndi wanga...Learn MorepopPhyzix