Song: Wife Material
Artist:  Phyzix
Year: 2021
Viewed: 38 - Published at: 9 years ago

[Verse 1: Phyzix]
Ndinapeza chi bhebhi anthu adziwe
Sindimachibisa sichapadziwe
Yemwe zikumuwawa adhiwe
Koma ichichi ndichanga chilindiwe
Sichingadzakupatse mphindi iwe
Chimakhala chili ndine udzimva iwe
Vito lake iweyo kudzimwa iwe
Umangogwila akaza openga ma byzwe
Za ife ndizokoma zothila kale
Sitimvetsana kuwawa, tsabola wa kale
Uyuyu ndi wanga si temporary
Ndikanena kuti ndimugaya simphale
Kutentha ngati nali samalani abale
Akusungila shuga onyambititsa mbale
Mkazi uyu ngoyiwalitsa abale
Amakomedetsa ngati anthu andale
Very good, very good

[Chorus: Pon G & Phyzix]
Mamie ndinu chi mkazi chowoneka bho
Mumachita kukhalangati a m'video
Mamie muli pure ngati kavitiko
Mukadzafuna banja ife tilipo
Ndinu wife material, 'terial, 'terial
Wife, ti-ti, ti-ti
Wife material, 'terial, 'terial
Wife, ti-ti, ti-ti
[Verse 2: Phyzix]
Ichi ndichindiwo koma si mpilu
Sindinachite kuchiba koma ndichi-deal
Ichi ndichibhebhi chadzadza feel
Dzina lake ndinaliyika kale pa wheel
Chimandikumbutsa [?]
Ma hope anga aku primary ku Mphungu
Tili ma nfana oyankhula chizungu
She had a chocolate skin, ndimamufila khungu
Chibhebhi changachi chandipatsa khungu
Ndikayenda ntaunimu sindiwona buthu
Ndadwala Chikondi teni pa teni
Chachita kundifika penpeni
Ndavomela mamie ndimalizeni
Sindipempha kuti "ambuye ndichilitseni"
Izi sizagulu, sizam'memo
Ineyo ndili momo m'menemomo

[Chorus: Pon G & Phyzix]
Mamie ndinu chi mkazi chowoneka bho
Mumachita kukhalangati a m'video
Mamie muli pure ngati kavitiko
Mukadzafuna banja ife tilipo
Ndinu wife material, 'terial, 'terial
Wife, ti-ti, ti-ti
Wife material, 'terial, 'terial
Wife, ti-ti, ti-ti
[Verse 3: Pon G & Phyzix]
Girl you de wife material
I just wanna make you my wife-oh
Girl you de one in a million
This feeling for you I can't deny
Iwe ndiwe mkazi wowoneka bho
Wowoneka bho, wowoneka bho
Iwe ndiwe chi mkazi chowoneka bho
Chowoneka bho, chowoneka bho
Iwe ndi mkazi o-fitter bho
O-fitter bho, o-fitter bho
Iwe ndichi mkazi cho-fitter bho
Cho-fitter bho, cho-fitter bho

[Chorus: Pon G & Phyzix]
Mamie ndinu chi mkazi chowoneka bho
Mumachita kukhalangati a m'video
Mamie muli pure ngati kavitiko
Mukadzafuna banja ife tilipo
Ndinu wife material, 'terial, 'terial
Wife, ti-ti, ti-ti
Wife material, 'terial, 'terial
Wife, ti-ti, ti-ti

[Outro: Pon G & Phyzix]
Ayi, ah (Ayi, kolokoto)
Mutu wanga zwe (Kolokoto)
Very good, very good
Very good, very good

( Phyzix )
www.ChordsAZ.com

TAGS :